Chewa translation

Ayah by Ayah

Tags

Download Links

Chewa translation translation for Surah Al-Qari'ah — Ayah 4

101:4
يَوۡمَ يَكُونُ ٱلنَّاسُ كَٱلۡفَرَاشِ ٱلۡمَبۡثُوثِ ٤
Limenelo ndi tsiku limene anthu adzakhala ngati agulugufe obalalika.1
Footnotes
  • [1] Apa, pakutanthauza kuti anthu adzakhala ali balalabalala ngati agulugufe ndipo azidzangodziponya uku ndi uku, osadziwa kopita. Imeneyo ndi nthawi yotuluka m’manda.