Chewa translation

Ayah by Ayah

Tags

Download Links

Chewa translation translation for Surah Al-Qari'ah — Ayah 6

101:6
فَأَمَّا مَن ثَقُلَتۡ مَوَٰزِينُهُۥ ٦
Tsono amene muyeso wake (wa zinthu zabwino) udzalemere (ndikupepuka zoipa).1
Footnotes
  • [1] Tsiku limenelo ntchito zonse zabwino ndi zoipa zidzayesedwa ndi muyeso wa Allah, koma sitidadziwitsidwe kuti muyeso umenewo udzakhala wotani udzayesa zonse zazikulu ndi zazing’ono zomwe mpaka za mumtima.