Chewa translation

Ayah by Ayah

Tags

Download Links

Chewa translation translation for Surah At-Takathur — Ayah 1

102:1
أَلۡهَىٰكُمُ ٱلتَّكَاثُرُ ١
Kwakutangwanitsani kusonkhanitsa (chuma chambiri ndi ana).1
Footnotes
  • [1] (Ndime 1-2) Ndi chizolowezi cha anthu kupikisana pa chuma ndi pa ana. Choncho, mma Ayah awa: 1-2 Allah akuwauza: Kupikisana kwawo kochuluka, kukonda za m’dziko kwambiri, kwaiwalitsa kutumikira Allah mpaka imfa kuwapeza.