Chewa translation

Ayah by Ayah

Tags

Download Links

Chewa translation translation for Surah At-Takathur — Ayah 3

102:3
كـَلَّا سَوۡفَ تَعۡلَمُونَ ٣
Sichoncho! Mudziwa posachedwapa.1
Footnotes
  • [1] Tanthauzo lake ndilakuti, pamene idzakufikirani imfa mudzadziwa kuti mudali kutaya nthawi ndi zinthu zopanda pake.