Chewa translation

Ayah by Ayah

Tags

Download Links

Chewa translation translation for Surah Al-'Asr — Ayah 1

103:1
وَٱلۡعَصۡرِ ١
Ndikuilumbilira nthawi.1
Footnotes
  • [1] Chinthu cha mtengo wapatali kwa munthu pa dziko lino ndi moyo wake. Choncho mphindi iliyonse imene akuigwiritsa ntchito pa zinthu zabwino ndiyo imene idzamuthandiza. Ndipo mphindi iliyonse imene akuigwiritsa ntchito mu zinthu zoipa kapena zopanda pake, kumeneko ndiko kutaika kwake; (kuluza).