Chewa translation

Ayah by Ayah

Tags

Download Links

Chewa translation translation for Surah Al-Kawthar — Ayah 2

108:2
فَصَلِّ لِرَبِّكَ وَٱنۡحَرۡ ٢
(Pakuti ndakupatsa zimenezo), pitiriza kupembedza Mbuye wako (moyera mtima) ndipo ipha nsembe yako (chifukwa chakuthokoza Allah pa zimene wakupatsa, monga ulemelero ndikukusankhira zabwino zambiri).1
Footnotes
  • [1] Tanthauzo loti “Mbuye wako yekha umupembedze” nkuti amupembedze Allah Yekha, asachite chiphamaso, asakhale monga amene amachita mapemphero ndi cholinga choti adzionetsere kwa anthu. Ndikutinso apereke nsembe m’dzina Lake, osati azimu ndi zina zotero.