Chewa translation

Ayah by Ayah

Tags

Download Links

Chewa translation translation for Surah An-Nasr — Ayah 2

110:2
وَرَأَيۡتَ ٱلنَّاسَ يَدۡخُلُونَ فِي دِينِ ٱللَّهِ أَفۡوَاجٗا ٢
Ndikuwaona anthu akulowa m’chipembedzo cha Allah ali magulumagulu,1
Footnotes
  • [1] Mneneri (s.a.w) pamene adalowa mu mzinda wa Makka ndi kugonjetsa adani ake monga momwe Allah adamulonjezera, a kafiri adali kubwera m’mafukomafuko kudzalowa m’chipembedzo cha Chisilamu.