Chewa translation

Ayah by Ayah

Tags

Download Links

Chewa translation translation for Surah Al-Masad — Ayah 5

111:5
فِي جِيدِهَا حَبۡلٞ مِّن مَّسَدِۭ ٥
Mkhosi mwake mdzamangidwa chingwe chopiringidwa bwino cha mlaza (chomlanga nacho).1
Footnotes
  • [1] Uyu mkazi wa Abu Lahab adali wodanitsa. Ntchito yake idali kutapa mawu uku, kuwapititsa uku, ncholinga chofuna kusokoneza.