Chewa translation

Ayah by Ayah

Tags

Download Links

Chewa translation translation for Surah An-Nas — Ayah 6

114:6
مِنَ ٱلۡجِنَّةِ وَٱلنَّاسِ ٦
Wochokera m’ziwanda ndi mwa anthu.”1
Footnotes
  • [1] Mchiyankhulo cha Chiarabu aliyense woipitsitsa amatchedwa “shaitan” satana, munthu kapena chiwanda. Satana wa muwanthu ndiwoipitsitsa kwambiri kwa anthu kuposa wa m’ziwanda.