Chewa translation

Ayah by Ayah

Tags

Download Links

Chewa translation translation for Surah An-Naba — Ayah 20

78:20
وَسُيِّرَتِ ٱلۡجِبَالُ فَكَانَتۡ سَرَابًا ٢٠
Ndipo mapiri adzachotsedwa m’malo mwake, adzakhala ngati zideruderu.1
Footnotes
  • [1] Apa, ndikuti zimene munthu amaziona patsogolo pake nkumaziganizira ngati madzi pomwe sali madzi. Choncho pa tsiku limenelo mapiri adzaoneka ngati akhazikika monga m’mene adalili pomwe sichoncho, adzakhala ngati thonje louluka ndi mphepo.