Chewa translation

Ayah by Ayah

Tags

Download Links

Chewa translation translation for Surah An-Naba — Ayah 22

78:22
لِّلطَّٰغِينَ مَـَٔابٗا ٢٢
Mbuto ya opyola malire.1
Footnotes
  • [1] Jahannam ndi dzina lamoto wodziwika wa tsiku lachimaliziro. Apa Allah akutidziwitsa kuti Jahannam ndi malo amene akudikira akafiri kuti m’menemo akalipidwe malipiro awo chifukwa chokanira aneneri pambuyo powasonyeza zizindikiro zoti iwo ndi aneneri a Allah. Ndiponso kumulakwira Allah pochita zimene adaletsa monga; kukana umodzi wa Allah, kukana utumiki wa Mahammad (s.a.w) ndi kukana uthenga wa Qur’an. Komanso kugwa mmachimo osiyanasiyana.