Chewa translation

Ayah by Ayah

Tags

Download Links

Chewa translation translation for Surah An-Nazi'at — Ayah 1

79:1
وَٱلنَّٰزِعَٰتِ غَرۡقٗا ١
Ndikulumbilira (angelo) amene amazula mwamphamvu (mizimu ya osakhulupirira).1
Footnotes
  • [1] (Ndime 1-5) M’Qur’an nthawi zambiri Allah amalumbilira zolengedwa Zake; zamoyo ndi zopanda moyo, zooneka ndi zosaoneka. Cholinga ndikutilimbikitsa kuti tikhale olingalira luso Lake pa chinthu chilichonse chimene wachilumbilira kuti tizindikire ulemelero Wake ndi mphamvu Zake zoposa.