Chewa translation

Ayah by Ayah

Tags

Download Links

Chewa translation translation for Surah An-Nazi'at — Ayah 33

79:33
مَتَٰعٗا لَّكُمۡ وَلِأَنۡعَٰمِكُمۡ ٣٣
(Adachita zonsezi) chifukwa chokusangalatsani inu ndi ziweto zanu.1
Footnotes
  • [1] Mu Ayah iyi Allah akusonyeza kuti Iye ndi Mwini mphamvu zonse zochitira chinthu chilichonse chachikulu kuposa kuwaukitsa akufa; ndiponso akukumbutsa ufulu Wake waukulu womwe adatichitira potipatsa zinthu zonsezo kuti tithandizike nazo.