Chewa translation

Ayah by Ayah

Tags

Download Links

Chewa translation translation for Surah 'Abasa — Ayah 38

80:38
وُجُوهٞ يَوۡمَئِذٖ مُّسۡفِرَةٞ ٣٨
Tsiku limenelo nkhope zina zidzakhala zowala;1
Footnotes
  • [1] (Ndime 38-39) Tsiku limenelo anthu adzakhala kakhalidwe ka mitundu iwiri: amene adakhulupilira ndi kuchita ntchito zabwino nkhope zawo zidzawala ndi chimwemwe, ndipo amene adakanira ndikumachita zoipa, nkhope zawo zidzakhala zafumbi ndi zakuda monga momwe anenera ma Ayah 40 ndi 42.