Chewa translation

Ayah by Ayah

Tags

Download Links

Chewa translation translation for Surah At-Takwir — Ayah 10

81:10
وَإِذَا ٱلصُّحُفُ نُشِرَتۡ ١٠
Ndi pamene makalata (momwe mudalembedwa zochita za aliyense) adzatambasulidwe ndi kugawidwa (kuti awerengedwe),1
Footnotes
  • [1] Awa ndi makalata achiwerengero momwe mwalembedwa zabwino za munthu ndi zoipa zake. Tsiku limenelo munthu aliyense adzapatsidwa yake kalata kuti aone iye mwini zoipa ndi zabwino zake.