Chewa translation

Ayah by Ayah

Tags

Download Links

Chewa translation translation for Surah At-Takwir — Ayah 12

81:12
وَإِذَا ٱلۡجَحِيمُ سُعِّرَتۡ ١٢
Ndi pamene Jahena idzasonkhezeredwe mwamphamvu,1
Footnotes
  • [1] (Ndime12-13) Tsiku limenelo Jannah idzayandikitsidwa kwa ochita zabwino ndiponso Moto udzayandikitsidwa kwa ochita zoipa kuti aone kumalo kwake.