Chewa translation

Ayah by Ayah

Tags

Download Links

Chewa translation translation for Surah At-Takwir — Ayah 22

81:22
وَمَا صَاحِبُكُم بِمَجۡنُونٖ ٢٢
Ndipo m’bale wanuyu siwamisala ayi.1
Footnotes
  • [1] (Ndime 22-25) Anthu okanira pamene adasowa chonena kwa mneneri (s.a.w) adali kunena nkhani zabodza kuti Mtumiki (s.a.w) wapenga ndikuti zomwe akuyankhula sadapatsidwe ndi Jibril.