Chewa translation

Ayah by Ayah

Tags

Download Links

Chewa translation translation for Surah Al-Mutaffifin — Ayah 10

83:10
وَيۡلٞ يَوۡمَئِذٖ لِّلۡمُكَذِّبِينَ ١٠
Chilango chaukali tsiku limenelo chili pa otsutsa,1
Footnotes
  • [1]

    Kutsutsa kulipo kwa mitundu itatu:

    (a) Kutsutsa kwa mawu ndi zochita;

    (b) Kutsutsa kwa zochita zokha, monga ukauzidwa kuti chinthu ichi nchoipa, munthu nkudziwa kuti zoona nchoipadi koma nkudzachichita chimenecho mosalabadira;

    (c) Kutsutsa ndi zolankhula zokha. Kumeneko ndiko monga munthu akudziwa kuti chakutichakuti ncholetsedwa (haramu) koma m’malo mwake iye nkumati chimenecho nchovomerezeka (halali)