Chewa translation

Ayah by Ayah

Tags

Download Links

Chewa translation translation for Surah Al-Inshiqaq — Ayah 17

84:17
وَٱلَّيۡلِ وَمَا وَسَقَ ١٧
Ndi usiku ndi zimene wasonkhanitsa,1
Footnotes
  • [1] Kubalalikana masana ndi chizolowezi cha anthu ndi nyama chifukwa chofunafuna zinthu zothandiza pa moyo wawo. Tsono usiku ukabwera amasonkhana ndi kukhala pamodzi. Ndipo ili ndilo tanthauzo la: “Usiku ndi zimene wasonkhanitsa.”