Chewa translation

Ayah by Ayah

Tags

Download Links

Chewa translation translation for Surah Al-Inshiqaq — Ayah 7

84:7
فَأَمَّا مَنۡ أُوتِيَ كِتَٰبَهُۥ بِيَمِينِهِۦ ٧
Tsono amene adzapatsidwe kaundula wa zochita zake kudzanja la manja,1
Footnotes
  • [1] Tsiku la chiweruziro munthu adzapatsidwa kaundula wake monga momwe zanenedwa mu Ayah 10 Surah Takwir, choncho ena adzapatsidwa ndi dzanja la kumanja; iwo ndiwo anthu abwino. Pomwe ena adzapatsidwa ndi dzanja la kumanzere, chakumbali yakumsana; iwowo ndiwo anthu oipa.