Chewa translation

Ayah by Ayah

Tags

Download Links

Chewa translation translation for Surah Al-Buruj — Ayah 4

85:4
قُتِلَ أَصۡحَٰبُ ٱلۡأُخۡدُودِ ٤
Atembeleredwa eni ngalande zamoto (zomwe adali kuwazunzira okhulupirira Allah, achimuna ndi achikazi).1
Footnotes
  • [1] Pamene Ayuda a ku Najrani adalowa m’Chikhristu, (Chisilamu chisadafike ndiponso Chikhristu chisadaonongeke), idamufika nkhaniyi mfumu yawo dzina lake Dhu-Nuwas; adabwera ku Najrani ndi gulu lankhondo lalikulu; adawakakamizira anthu ku Chiyuda koma iwo adakana. Nayamba kuwapha anthu okhulupilirawo powaponya m’ngalande za moto.