Chewa translation

Ayah by Ayah

Tags

Download Links

Chewa translation translation for Surah Al-A'la — Ayah 14

87:14
قَدۡ أَفۡلَحَ مَن تَزَكَّىٰ ١٤
Ndithu wapambana amene wadziyeretsa (ku machimo),1
Footnotes
  • [1] Tanthauzo lake ndikuti amene wadziyeretsa posiya kumuphatikiza Allah ndi zolengedwa ndi kumchimwira ndi machimo onse. Machimo amaletsa ulaliki wabwino kulowa mu mtima wa munthu. (yang’anani ndemanga ya 14 mu surat ya Al-Mutaffifin).