Chewa translation

Ayah by Ayah

Tags

Download Links

Chewa translation translation for Surah Al-A'la — Ayah 18

87:18
إِنَّ هَٰذَا لَفِي ٱلصُّحُفِ ٱلۡأُولَىٰ ١٨
Ndithu izi (mukuuzidwa m’Qur’an) zilipo m’mabuku oyamba, akale,1
Footnotes
  • [1] Mawu akuti “wapambana amene wadziyeretsa ndi kumkumbukira Mbuye wake ndi kumapemphera,” ndiponso kuti: “ tsiku lachimaliziro ndilabwino kuposa dziko lapansi” mawuwa adanenedwanso m’mabuku oyamba; sikuti Qur’an ndiyo yayamba kunena zimenezi.