Chewa translation

Ayah by Ayah

Tags

Download Links

Chewa translation translation for Surah Al-Ghashiyah — Ayah 12

88:12
فِيهَا عَيۡنٞ جَارِيَةٞ ١٢
Mmenemo muli kasupe woyenda (mokongola).1
Footnotes
  • [1] (Ndime 12-16) Zosangalatsa zenizeni za tsiku lachimaliziro monga momwe adatiuzira Mneneri (s.a.w) kuti ku Jannah kuli zinthu zimene diso silidapenyepo ngakhale khutu silidamvepo ndipo sizidapitepo m’maganizo a munthu. Choncho zokondweretsa izi zimene Allah watiuza apa akungofanizira ndi zinthu zomwe tikuzidziwa.