Chewa translation

Ayah by Ayah

Tags

Download Links

Chewa translation translation for Surah Al-Ghashiyah — Ayah 2

88:2
وُجُوهٞ يَوۡمَئِذٍ خَٰشِعَةٌ ٢
Nkhope zina tsiku limenelo, zidzakhala zonyozeka,1
Footnotes
  • [1] Tanthauzo la nkhope apa ndi eni nkhopezo. Amene akunenedwa pamenepa ndi anthu oipa. Allah watchula nkhope chifukwa ndi chiwalo cholemekezeka pa chilengedwe cha munthu ndipo ndi pamene pali chithunzi chake.