Chewa translation

Ayah by Ayah

Tags

Download Links

Chewa translation translation for Surah Al-Ghashiyah — Ayah 9

88:9
لِّسَعۡيِهَا رَاضِيَةٞ ٩
Zidzakondwera ndi malipiro a zochita zake (za pa dziko lapansi).1
Footnotes
  • [1] Tanthauzo la “kukondweretsedwa ndi zochita zawo’’ ndikuti anthu abwino adzakondwera ndi ntchito zawo zabwino zomwe adazichita pa dziko lapansi akadzakhala ndi malipiro abwino pa tsiku lachimaliziro.