Chewa translation

Ayah by Ayah

Tags

Download Links

Chewa translation translation for Surah Al-Fajr — Ayah 14

89:14
إِنَّ رَبَّكَ لَبِٱلۡمِرۡصَادِ ١٤
Ndithu Mbuye wako ali tcheru (ndi zochita za anthu. Ndipo akuwasungira kuti adzawalipire).1
Footnotes
  • [1] Apa ndikuti Allah akuwaona anthu Ake nthawi ili yonse. Palibe chimene iwo achita popanda Iye kuchiona ndi kuchilemba.