Chewa translation

Ayah by Ayah

Tags

Download Links

Chewa translation translation for Surah Al-Fajr — Ayah 7

89:7
إِرَمَ ذَاتِ ٱلۡعِمَادِ ٧
Aku Irama; ataliatali ngati zipilala.1
Footnotes
  • [1] (Ndime 7-9) Âdi aku Irama ndi mtundu wa Mneneri Hud. Adali akuluakulu matupi a mphamvu kwambiri mwakuti ankanena kuti: “Ndani wamphamvu kuposa ife!” Thamudu (Samudu) ndi mtundu wa Mneneri Swaleh. Iwowa adali kukhala ku mpoto kwa chilumba cha Arabia.