Chewa translation

Ayah by Ayah

Tags

Download Links

Chewa translation translation for Surah Al-Balad — Ayah 11

90:11
فَلَا ٱقۡتَحَمَ ٱلۡعَقَبَةَ ١١
Kodi walikwera phiri lovutalo (lomwe lingakamfikitse ku Jannah)?1
Footnotes
  • [1] Tanthauzo lake ndikuti bwanji munthu sathokoza chifundo chimenechi (chopatsidwa maso ndi pakamwa) pogwiritsa ntchito chuma chake pa zinthu zabwino zimene Allah wazitchula m’ma Ayah akubwerawa? Ndipo tanthauzo la “kukwera phiri lovuta’’ ndiko kupereka chuma panjira ya Allah chimene chili ndinthu chovuta kwa anthu ambiri ndipo chimafanana ndikukwera phiri losongoka.