Chewa translation

Ayah by Ayah

Tags

Download Links

Chewa translation translation for Surah Al-Layl — Ayah 19

92:19
وَمَا لِأَحَدٍ عِندَهُۥ مِن نِّعۡمَةٖ تُجۡزَىٰٓ ١٩
Ndipo palibe aliyense kwa iye, amene adamchitira za chifundo zomwe zikulipidwa.1
Footnotes
  • [1] (Ndime 19-20)Tanthauzo la ma Ayah awiriwa nkuti munthu uyu sakupereka chuma chake chifukwa chobwezera chifundo cha anthu, kapena kuti adzamubwezerenso iye chifundo, koma akupereka chifukwa chofuna chikondi cha Mbuye wake basi.