Chewa translation

Ayah by Ayah

Tags

Download Links

Chewa translation translation for Surah Al-Layl — Ayah 4

92:4
إِنَّ سَعۡيَكُمۡ لَشَتَّىٰ ٤
Ndithu zochita zanu nzosiyanasiyana.1
Footnotes
  • [1] Tanthauzo lake ndikuti mwa anthu alipo ena amene amachita zabwino ndipo ena amachita zoipa. Ena amagwira ntchito zothandiza pambuyo pa imfa pamodzi ndi kutumikira Allah. Ndipo pali ena omwe amangokhala otanganidwa ndi zadziko lapansi. Ena amachita zinthu zopindula pomwe ena satero.