Chewa translation

Ayah by Ayah

Tags

Download Links

Chewa translation translation for Surah Ad-Duhaa — Ayah 3

93:3
مَا وَدَّعَكَ رَبُّكَ وَمَا قَلَىٰ ٣
Sadakusiye Mbuye wako (iwe Mneneri) (s.a.w) ndiponso sadakude.1
Footnotes
  • [1] M’masiku oyamba pa chiyambi cha Usilamu, padapita masiku angapo Mtumiki (s.a.w) osamutsikira chivumbulutso. Iye poona izi adali kukaika ndi kudandaula kwakukulu, nao okanira a pa Makka adali kumchita chipongwe. Adali kumunena kuti: “Kodi Mbuye wako wakusiya kapena wakukwiira?’’ Basi apa Allah akumutonthoza Mneneri Wake, pamodzi ndi kuwayankha okanira aja kuti: “Sadamusiye ndipo sadakwiye naye.”