Chewa translation

Ayah by Ayah

Tags

Download Links

Chewa translation translation for Surah At-Tin — Ayah 5

95:5
ثُمَّ رَدَدۡنَٰهُ أَسۡفَلَ سَٰفِلِينَ ٥
Pambuyo pake tamubwezera pansi kumposa wa pansi.1
Footnotes
  • [1] Munthu ali ndi makhalidwe awiri: Ngati agwiritsa ntchito nzeru zake amaongoka ndipo amaiposa nyama ili yonse. Koma ngati sagwiritsa ntchito nzeru zake amasokera ndi kukhala wapansi kuposa nyama zonse.