Chewa translation

Ayah by Ayah

Tags

Download Links

Chewa translation translation for Surah Al-Qadr — Ayah 5

97:5
سَلَٰمٌ هِيَ حَتَّىٰ مَطۡلَعِ ٱلۡفَجۡرِ ٥
Mtendere usiku umenewo! (Palibe mavuto ndi zoipa) mpaka m’bandakucha.1
Footnotes
  • [1] Adanena Baidawi kuti tanthauzo la Ayah iyi ndikuti mu usiku umenewu Allah amalamula kuti kukhale mtendere wokhawokha. Koma mu usiku wina amalamula kuti kukhale mtendere ndi masoka.