Chewa translation

Ayah by Ayah

Tags

Download Links

Chewa translation translation for Surah Az-Zalzalah — Ayah 7

99:7
فَمَن يَعۡمَلۡ مِثۡقَالَ ذَرَّةٍ خَيۡرٗا يَرَهُۥ ٧
Choncho, amene angachite chabwino cholemera ngati kanjere kakang’ono, adzaona malipiro ake.1
Footnotes
  • [1] (Ndime 7-8) Ma Ayah awiriwa akutidziwitsa kuti munthu adzalipidwa pa chilichonse chimene akuchita, chabwino kapena choipa, ngakhale chikhale chochepa monga kulemera kwa kanjere kochepa kwambiri.