Chewa translation

Ayah by Ayah

Tags

Download Links

Chewa translation translation for Surah Ar-Rum — Ayah 1

30:1
الٓمٓ ١
Alif-Lâm-Mîm.1
Footnotes
  • [1] Surayi yayamba ndi zilembo za alifabeti posonyeza kuti Qur’an yalembedwa kupyolera m’malemba amenewa omwe Arabu amawayankhula mofewa. Koma Aquraish adalephera kulemba Buku limeneli pomwe malembo ake akuwadziwa.