Chewa translation

Ayah by Ayah

Tags

Download Links

Chewa translation translation for Surah Al-Ahzab — Ayah 42

33:42
وَسَبِّحُوهُ بُكۡرَةٗ وَأَصِيلًا ٤٢
Ndipo mulemekezeni m’mawa ndi madzulo.1
Footnotes
  • [1] Allah wasankha nthawi ziwiri kuti zikhale zochulukitsa kumtamanda ndi kumulemekeza chifukwa chakuti zimenezi ndi nthawi zabwino zimene angelo amatsika kuchokera kumwamba.