Chewa translation

Ayah by Ayah

Tags

Download Links

Chewa translation translation for Surah Ya-Sin — Ayah 42

36:42
وَخَلَقۡنَا لَهُم مِّن مِّثۡلِهِۦ مَا يَرۡكَبُونَ ٤٢
Ndipo tidawapangira chonga icho chomwe akuchikwera.1
Footnotes
  • [1] Allah ndi Yemwe adapanga zombo ngakhale kuti zidapangidwa ndi manja a anthu, chifukwa Iye ndi Amene adaphunzitsa anthu kupanga zombozo.