Resources
Tools
Docs
Community
FAQ
Github
Login
CMS
Resources
Tools
Docs
Credits
Community
FAQ
Github
Login
Developer Resources
Translations
Chewa translation
Chewa translation
Ayah by Ayah
Tags
Translation
Chichewa
chewa
nyanja
Download Links
Download simple.json
Download simple.sqlite
Preview
Docs
Licence
A translation of every ayah of the Quran in Chichewa, Chewa, Nyanja.
Chewa translation translation for Surah Al-Jumu'ah — Ayah 5
Jump to Ayah
[]
← Previous
Next →
62:5
مَثَلُ ٱلَّذِينَ حُمِّلُواْ ٱلتَّوۡرَىٰةَ ثُمَّ لَمۡ يَحۡمِلُوهَا كَمَثَلِ ٱلۡحِمَارِ يَحۡمِلُ أَسۡفَارَۢاۚ بِئۡسَ مَثَلُ ٱلۡقَوۡمِ ٱلَّذِينَ كَذَّبُواْ بِـَٔايَٰتِ ٱللَّهِۚ وَٱللَّهُ لَا يَهۡدِي ٱلۡقَوۡمَ ٱلظَّٰلِمِينَ ٥
Fanizo la (Ayuda) amene adawasenzetsa Taurat (pokakamizidwa kuti atsatire zophunzitsa za bukulo, koma osatsatira), ali ngati bulu amene akusenza mabuku akuluakulu anzeru, (koma osathandizika nawo). Taonani kuipa fanizo la anthu amene atsutsa zisonyezo za Allah. Ndipo Allah saongola anthu achinyengo.
1
Footnotes
[1]
Allah Wotukuka, akufanizira Ayuda amene amadziwa kuwerenga Taurat bwinobwino, koma zomwe akuwerengazo osazigwiritsa ntchito, ngati bulu wosenza mabuku akuluakulu popanda chopeza pomwe mabukuwo ali odzaza ndi zinthu zabwino zophunzitsa nzeru zabwino.
Loading…
Loading…