Chewa translation

Ayah by Ayah

Tags

Download Links

Chewa translation translation for Surah An-Naba — Ayah 3

78:3
ٱلَّذِي هُمۡ فِيهِ مُخۡتَلِفُونَ ٣
Imene iwo akusiyana (maganizo).1
Footnotes
  • [1] Nkhani yaikulu imene akafiri (anthu osakhulupilira Allah) adali kufunsana wina ndi mnzake ndi nkhani yakuuka tsiku la Qiyâma ndi uneneri wa Mtumiki Muhammad. Amafunsana kuti, “Kodi nzoona tidzauka m’manda, nanga nzoona kuti Muhammad ndi Mneneri?” Adali kufunsananso kuti, “Kodi zakuti Allah ndi Mmodzi ndi zoona?”