Chewa translation

Ayah by Ayah

Tags

Download Links

Chewa translation translation for Surah An-Naba — Ayah 4

78:4
كـَلَّا سَيَعۡلَمُونَ ٤
Aleke (zimenezo) adzadziwa posachedwapa.1
Footnotes
  • [1] Kuyankhula koti: “Kallaa” kwanenedwa kwambiri m’Qur’an. Tanthauzo lake nthawi zina ndikuletsa, nthawi zina ndikutsimikiza. Choncho mawuwa amatanthauzidwa malinga ndi momwe chiganizocho chilili.