Chewa translation

Ayah by Ayah

Tags

Download Links

Chewa translation translation for Surah At-Takwir — Ayah 1

81:1
إِذَا ٱلشَّمۡسُ كُوِّرَتۡ ١
Pamene dzuwa lidzakulungidwe (ndikuchotsedwa kuwala kwake),1
Footnotes
  • [1] Surah zambiri zimene zidavumbulutsidwa ku Makka zimanena zododometsa za tsiku lachimaliziro.