Chewa translation

Ayah by Ayah

Tags

Download Links

Chewa translation translation for Surah At-Takwir — Ayah 4

81:4
وَإِذَا ٱلۡعِشَارُ عُطِّلَتۡ ٤
Ndi pamene ngamira zabere lamiyezi khumi zidzasiidwe (zopanda oziyang’anira),1
Footnotes
  • [1] Ngamira za bere ndi chuma cha mtengo wapatali kwa Aarabu. Akuuzidwa apa kuti tsiku limenelo adzazisiya osazilabadira konse.