Chewa translation

Ayah by Ayah

Tags

Download Links

Chewa translation translation for Surah At-Takwir — Ayah 5

81:5
وَإِذَا ٱلۡوُحُوشُ حُشِرَتۡ ٥
Ndi pamene nyama za mtchire zidzasonkhanitsidwe pamodzi (kuchokera mmalo osiyanasiyana chifukwa chakuopsa kwakukulu kwa tsikulo),1
Footnotes
  • [1] Mwa zina zododometsa pa tsiku limenelo ndi nyama za mtchire kusonkhanitsidwa pamodzi popanda kumenyana kapena kudyana.