Chewa translation

Ayah by Ayah

Tags

Download Links

Chewa translation translation for Surah Al-A'la — Ayah 8

87:8
وَنُيَسِّرُكَ لِلۡيُسۡرَىٰ ٨
Ndipo tikufewetsera (njira yochitira zinthu) zabwino.1
Footnotes
  • [1] Tanthauzo la ‘kufewetsa’ ndiko kuti Shariya ya Chisilamu (malamulo) siili yovuta kuyikwaniritsa monga momwe adalili malamulo a zipembedzo zoyamba. Ndipo ndi malamulo othandiza anthu onse, nthawi zonse ndi pamalo paliponse.