Chewa translation

Ayah by Ayah

Tags

Download Links

Chewa translation translation for Surah Al-A'la — Ayah 9

87:9
فَذَكِّرۡ إِن نَّفَعَتِ ٱلذِّكۡرَىٰ ٩
Choncho akumbutse (wanthu powalalikira) ngati kukumbutsa kuthandiza.1
Footnotes
  • [1] Tanthauzo la apa sikuti Mtumiki (s.a.w) alalikire pokhapokha waona kuti ulalikiwo uthandiza ayi, koma alalikire ndithu kaya kulalikirako kuthandiza kapena ayi, monga momwe zalongosolera Ayah zotsatirazi. Kuyankhula kotere, Arabu amakutcha “iktifa.”