Chewa translation

Ayah by Ayah

Tags

Download Links

Chewa translation translation for Surah Al-Fajr — Ayah 12

89:12
فَأَكۡثَرُواْ فِيهَا ٱلۡفَسَادَ ١٢
Ndipo adachulukitsa m’menemo kuononga (pamwamba pa kuononga).1
Footnotes
  • [1] Mzinthu zoipa zimene Farawo adachita, ndi kudzitcha kuti iye ndi mulungu, kupha ana achimuna popanda chilungamo, ndi kuwazunza Aisraeli.