Chewa translation

Ayah by Ayah

Tags

Download Links

Chewa translation translation for Surah Al-Fajr — Ayah 27

89:27
يَٰٓأَيَّتُهَا ٱلنَّفۡسُ ٱلۡمُطۡمَئِنَّةُ ٢٧
E iwe mzimu wokhazikika (ndi choona)!1
Footnotes
  • [1] “Mzimu wokhazikika” ndi mzimu wa munthu wokhulupilira amene akuchita zomwe walamulidwa ndi kusiya zimene waletsedwa. Umenewo ndiwo mzimu umene udzakhale wodekha pa tsiku lachimaliziro chifukwa chakuti pa tsikulo sudzakhala ndi mantha kapena kudandaula.