Chewa translation

Ayah by Ayah

Tags

Download Links

Chewa translation translation for Surah Ash-Shams — Ayah 9

91:9
قَدۡ أَفۡلَحَ مَن زَكَّىٰهَا ٩
Ndithu wapambana amene wauyeretsa.1
Footnotes
  • [1] Kuyeretsa mzimu ndiko kuukongoletsa ndi maphunziro ndi ntchito zabwino. Zimenezi ndizo zimamkwanitsa munthu kuti atchulidwe munthu. Ndipo zimenezi ndizo zingapereke ulemelero kwa munthu pa dziko mpaka pa tsiku lachimaliziro.