Chewa translation

Ayah by Ayah

Tags

Download Links

Chewa translation translation for Surah Ash-Shams — Ayah 10

91:10
وَقَدۡ خَابَ مَن دَسَّىٰهَا ١٠
Ndipo ndithu wataika amene wauononga.1
Footnotes
  • [1] Kuwuononga mzimu ndiko kuuchitira mphwayi; kungoulekelera ndikumautsatira pa zimene ufuna mpaka kulowa mu uve ndi m’machimo a umbuli ndipo ndi kuonongeka pa dziko lino mpaka pa tsiku lachimaliziro.